Tag: #MP Roseby Gadama

10
Oct

Zomba-Thondwe Prayer Day

Phungu wa nyumba ya malamulo ku Zomba Thondwe, a Roseby Gadama, wapereka ndalama zokwanira K1 million kwacha kuti ithandize ntchito zampingo. A Gadama ndi mlendo olemekezeka pa mwambo wa mapemphero omwe akuchitika pansi pa utsogoleri wa m’mipingo wa Pastors Fraternal yaku Nasawa, Thondwe, Dzaone ndi Mayaka m’boma la Zomba. Iwo ati achita izi ngati njira imodzi yosangalalira kubadwa kwawo pa

Read more